2 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira. 2 Mbiri 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima n’kutsogolera anthu ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha ana a Seiri+ okwana 10,000.+
20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira.
11 Ndiyeno Amaziya analimba mtima n’kutsogolera anthu ake kupita kuchigwa cha Mchere.+ Kumeneko anapha ana a Seiri+ okwana 10,000.+