Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 35:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pamenepo Neko anatumiza anthu kwa iye kukamuuza kuti: “Kodi ndili nawe chiyani iwe mfumu ya Yuda? Lero sindinabwere kudzamenyana ndi iweyo. Ndabwera kudzamenyana ndi mtundu wina umene Mulungu wanena kuti ndikauwopseze. Ngati ukufuna kuti zinthu zikuyendere bwino, usachite zimenezi. Uope Mulungu amene ali nane ndipo usalole kuti iye akuwononge.”+

  • Miyambo 3:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Usakangane ndi munthu popanda chifukwa,+ ngati sanakuchitire choipa.+

  • Miyambo 20:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kuleka kukangana kumabweretsa ulemerero kwa munthu,+ koma aliyense wopusa amafulumira kuyambitsa mkangano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena