2 Mbiri 25:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ukunena kuti wagonjetsa Edomu,+ choncho mtima wako+ wayamba kudzikuza ndi kudzitamandira.+ Khala m’nyumba mwako momwemo.+ N’chifukwa chiyani ukufuna kumenya nkhondo pamene uli wofooka?+ Iweyo ndi Ayuda amene uli nawowo mugonja.”+ Miyambo 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+
19 Ukunena kuti wagonjetsa Edomu,+ choncho mtima wako+ wayamba kudzikuza ndi kudzitamandira.+ Khala m’nyumba mwako momwemo.+ N’chifukwa chiyani ukufuna kumenya nkhondo pamene uli wofooka?+ Iweyo ndi Ayuda amene uli nawowo mugonja.”+
12 Wochenjera amene waona tsoka amabisala.+ Koma anthu osadziwa zinthu amene amangopitabe amalangidwa.+