2 Mbiri 26:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Koma Uziya anakwiya kwambiri+ atanyamula chiwaya chofukizira+ m’manja mwake. Atawakwiyira choncho ansembewo, khate+ linabuka+ pamphumi pake ali pamaso pa ansembewo m’nyumba ya Yehova pambali pa guwa lansembe zofukiza. Yobu 34:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+
19 Koma Uziya anakwiya kwambiri+ atanyamula chiwaya chofukizira+ m’manja mwake. Atawakwiyira choncho ansembewo, khate+ linabuka+ pamphumi pake ali pamaso pa ansembewo m’nyumba ya Yehova pambali pa guwa lansembe zofukiza.
19 Alipo amene sanakonderepo akalonga,Ndipo saganizira kwambiri wolemekezeka kuposa wonyozeka,+Chifukwa onsewo anapangidwa ndi manja ake.+