2 Mafumu 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 M’chaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi+ mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya, kwa zaka 17. 2 Mafumu 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’chaka cha 37 cha Yehoasi+ mfumu ya Yuda, Yehoasi mwana wa Yehoahazi anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 16. 2 Mafumu 14:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 M’chaka cha 15 cha Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, Yerobowamu+ mwana wa Yehoasi mfumu ya Isiraeli anakhala mfumu ku Samariya, ndipo analamulira zaka 41. 2 Mafumu 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pomalizira pake, Yerobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake, mafumu a Isiraeli, ndipo Zekariya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
13 M’chaka cha 23 cha Yehoasi+ mwana wa Ahaziya+ mfumu ya Yuda, Yehoahazi+ mwana wa Yehu+ anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya, kwa zaka 17.
10 M’chaka cha 37 cha Yehoasi+ mfumu ya Yuda, Yehoasi mwana wa Yehoahazi anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 16.
23 M’chaka cha 15 cha Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, Yerobowamu+ mwana wa Yehoasi mfumu ya Isiraeli anakhala mfumu ku Samariya, ndipo analamulira zaka 41.
29 Pomalizira pake, Yerobowamu anagona pamodzi ndi makolo ake, mafumu a Isiraeli, ndipo Zekariya+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.