Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Choncho anasankha mizinda ina kuti ikhale yopatulika. Mizinda yake inali Kedesi+ ku Galileya m’dera lamapiri la Nafitali, Sekemu+ m’dera lamapiri la Efuraimu, Kiriyati-ariba,+ kutanthauza Heburoni, m’dera lamapiri la Yuda.

  • 1 Mafumu 9:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mfumu Solomo anapatsa Hiramu mizinda 20 m’dera la Galileya.+ (Hiramu+ mfumu ya Turo anathandiza Solomo+ ndi matabwa a mkungudza, matabwa a mitengo yofanana ndi mkungudza, ndi golide yense amene anafuna.)+

  • Yesaya 9:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Komabe mdima wake sudzakhala ngati wa pa nthawi imene dzikolo linali m’masautso, ngati kale pamene anthu ankanyoza dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali.+ Koma patsogolo pake anthu analilemekeza dzikolo,+ dera limene kuli njira ya m’mphepete mwa nyanja, m’chigawo cha Yorodano, ku Galileya kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina.+

  • Mateyu 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Anthu okhala m’dziko la Zebuloni ndi dziko la Nafitali, m’mbali mwa msewu wa kunyanja kutsidya lina la Yorodano, ku Galileya+ kumene kunali kukhala anthu a mitundu ina,

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena