Genesis 31:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+ Ekisodo 34:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pakuti ndidzathamangitsira mitunduyo kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakuza dera lanu.+ Palibe aliyense adzasirira dziko lanu pamene mwachoka kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka.+ Yeremiya 15:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova wanena kuti: “Ndithu, ndidzakuchitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzakuthandiza kuti ndikupulumutse kwa adani ako pa nthawi ya tsoka+ ndi nthawi ya nsautso.+ Aroma 8:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+
24 Koma usiku m’maloto,+ Mulungu anafikira Labani Msiriyayo+ n’kumuuza kuti: “Samala kuti usanene chilichonse chosokoneza zochita za Yakobo.”+
24 Pakuti ndidzathamangitsira mitunduyo kutali ndi inu,+ ndipo ndidzakuza dera lanu.+ Palibe aliyense adzasirira dziko lanu pamene mwachoka kukaona nkhope ya Yehova Mulungu wanu katatu pa chaka.+
11 Yehova wanena kuti: “Ndithu, ndidzakuchitira zinthu zabwino+ ndipo ndidzakuthandiza kuti ndikupulumutse kwa adani ako pa nthawi ya tsoka+ ndi nthawi ya nsautso.+
31 Ndiye tinene kuti chiyani pa zinthu zimenezi? Ngati Mulungu ali kumbali yathu, ndani adzatsutsana nafe?+