Akolose 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tikupemphereranso kuti muziyenda mogwirizana ndi zimene Yehova+ amafuna,+ kuti muzimukondweretsa pa chilichonse,+ pamene mukupitiriza kubala zipatso m’ntchito iliyonse yabwino, ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+ 1 Petulo 3:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso. 1 Yohane 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+
10 Tikupemphereranso kuti muziyenda mogwirizana ndi zimene Yehova+ amafuna,+ kuti muzimukondweretsa pa chilichonse,+ pamene mukupitiriza kubala zipatso m’ntchito iliyonse yabwino, ndi kuwonjezera kumudziwa Mulungu molondola.+
9 Osabwezera choipa pa choipa+ kapena chipongwe pa chipongwe,+ koma m’malomwake muzidalitsa,+ chifukwa anakuitanirani njira ya moyo imeneyi, kuti mudzalandire dalitso.
22 ndipo chilichonse chimene tingapemphe, iye adzatipatsa,+ chifukwa tikusunga malamulo ake ndi kuchita zinthu zomukondweretsa.+