-
1 Mbiri 22:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Kenako Davide anati: “Mwana wanga Solomo ndi wamng’ono komanso wosakhwima,+ koma nyumba yoti adzamangire Yehova idzakhala yokongola,+ yaulemerero wosaneneka+ ndiponso yotchuka ndi yotamandika kumayiko onse. Ndiyetu ndim’konzere zipangizo zoti adzagwiritsire ntchito.” Chotero Davide asanafe, anasonkhanitsa zipangizo zambirimbiri pokonzekera ntchitoyo.+
-