Deuteronomo 12:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani. 2 Mbiri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino+ zimene Yehova anachitira Davide, Solomo, ndiponso zimene anachitira anthu ake Aisiraeli.+ Nehemiya 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya+ ndi kukondwera kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+
7 Kumalo amenewo, inuyo ndi mabanja anu muzidzadya zimenezi ndi kusangalala ndi zochita zanu zonse+ pamaso pa Yehova,+ chifukwa Yehova Mulungu wanu wakudalitsani.
10 Pa tsiku la 23 la mwezi wa 7, Solomo anauza anthuwo kuti azipita kwawo. Iwo anapita akusangalala+ komanso akumva bwino mumtima, chifukwa cha zabwino+ zimene Yehova anachitira Davide, Solomo, ndiponso zimene anachitira anthu ake Aisiraeli.+
12 Choncho anthu onse anapita kukadya, kukamwa, kukagawira ena chakudya+ ndi kukondwera kwambiri+ chifukwa anamvetsa bwino mawu amene anawafotokozera.+