Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Iwo anapitiriza kuwerenga+ bukulo mokweza. Anapitiriza kuwerenga chilamulo cha Mulungu woona, kuchifotokozera ndi kumveketsa tanthauzo lake. Iwo anapitiriza kuthandiza anthuwo kumvetsa tanthauzo la zimene anali kuwerenga.+

  • Salimo 119:130
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 130 Kuululidwa kwa mawu anu kumapereka kuwala,+

      Kumathandiza anthu osadziwa zambiri kukhala ozindikira.+

  • Miyambo 2:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Nzeru zikalowa mumtima mwako,+ ndipo kudziwa zinthu kukakhala kosangalatsa m’moyo wako,+

  • Luka 24:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Iwo anayamba kuuzana kuti: “Kodi si paja mitima yathu inali kunthunthumira pamene anali kulankhula nafe mumsewu, ndi kutifotokozera Malemba momveka bwino?”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena