1 Mbiri 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli yense+ ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo kwa anthu ake onse.+ Salimo 78:71 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+
14 Davide anapitiriza kulamulira Isiraeli yense+ ndipo nthawi zonse anali kupereka zigamulo ndi kuchita chilungamo kwa anthu ake onse.+
71 Anamutenga kumene anali kuweta nkhosa zoyamwitsa,+Anamutenga kuti akhale m’busa wa ana a Yakobo amene ndi anthu ake,+Ndi Isiraeli, amene ndi cholowa chake.+