1 Mbiri 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Sesani+ analibe ana aamuna, koma anali ndi ana aakazi. Iye anali ndi wantchito wachiiguputo+ dzina lake Yaha.
34 Sesani+ analibe ana aamuna, koma anali ndi ana aakazi. Iye anali ndi wantchito wachiiguputo+ dzina lake Yaha.