1 Mbiri 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Mwana wa Apaimu anali Isi, mwana wa Isi anali Sesani,+ mwana wa Sesani anali Alai.