Oweruza 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+ 1 Mbiri 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Reyaya+ mwana wa Sobala anabereka Yahati. Yahati anabereka Ahumai ndi Lahadi. Amenewa ndiwo anali mabanja a Azorati.+
2 Pa nthawiyi panali mwamuna wina wa ku Zora+ wa fuko la Dani,+ ndipo dzina lake anali Manowa.+ Mkazi wake anali wosabereka, moti analibe mwana.+
2 Reyaya+ mwana wa Sobala anabereka Yahati. Yahati anabereka Ahumai ndi Lahadi. Amenewa ndiwo anali mabanja a Azorati.+