Rute 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”
10 Komanso ndikugula Rute Mmowabu, mkazi wa Maloni, kukhala mkazi wanga kuti dzina la mwamuna wake amene anamwalira+ libwerere pacholowa chake, kutinso lisafafanizike pakati pa abale ake ndi mumzinda wathu. Inu ndinu mboni+ lero.”