Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 2:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Ana a Isiraeli sanamvere ngakhale oweruza awo, koma anachita chiwerewere+ ndi milungu ina+ ndi kuigwadira. Iwo anapatuka mwamsanga panjira imene makolo awo anayendamo. Makolo awo anayenda m’njira imeneyo mwa kumvera malamulo a Yehova,+ koma iwo sanachite mofanana ndi makolo awo.

  • Oweruza 8:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Ndiyeno zinachitika kuti Gidiyoni atangomwalira, ana a Isiraeli anayambanso kupembedza Abaala,+ moti anaika Baala-beriti* kukhala mulungu wawo.+

  • 2 Mafumu 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iwo anapitiriza kudziikira zipilala zopatulika+ ndi mizati yopatulika+ paphiri lililonse lalitali,+ ndi pansi pa mtengo uliwonse waukulu wa masamba obiriwira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena