Ekisodo 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno mlongo wake wa mwanayo anaima chapatali ndithu kuti aone zimene zingachitikire mwanayo.+ Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+ Numeri 12:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+
10 Kenako mtambo uja unachoka pamwamba pa chihemacho. Pomwepo, Miriamu anagwidwa ndi khate loyera mbuu!+ Aroni atacheuka, anangoona kuti Miriamu wachita khate.+