1 Mbiri 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ana a Bela+ analipo asanu: Eziboni, Uzi, Uziyeli, Yerimoti, ndi Iri. Iwo anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, amuna amphamvu ndi olimba mtima, ndipo pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo,+ analipo 22,034.
7 Ana a Bela+ analipo asanu: Eziboni, Uzi, Uziyeli, Yerimoti, ndi Iri. Iwo anali atsogoleri a nyumba ya makolo awo, amuna amphamvu ndi olimba mtima, ndipo pamndandanda wa mayina wotsatira makolo awo,+ analipo 22,034.