Genesis 30:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Rakele anati: “Nayu kapolo wanga Biliha.+ Mugone naye kuti andiberekere mwana woti akhale wanga,* kuti ineyonso ndikhale ndi ana kuchokera kwa iye.”+ Genesis 35:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12. Genesis 46:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Amenewa ndiwo anali ana a Biliha,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Rakele. Awa ndiwo ana amene Biliha anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 7.
3 Kenako Rakele anati: “Nayu kapolo wanga Biliha.+ Mugone naye kuti andiberekere mwana woti akhale wanga,* kuti ineyonso ndikhale ndi ana kuchokera kwa iye.”+
22 Isiraeli atamanga msasa+ m’dziko limenelo, Rubeni anagona ndi Biliha mkazi wamng’ono* wa bambo ake, ndipo Isiraeli anamva zimene zinachitikazo.+ Yakobo anali ndi ana aamuna 12.
25 Amenewa ndiwo anali ana a Biliha,+ yemwe Labani anam’pereka kwa mwana wake wamkazi Rakele. Awa ndiwo ana amene Biliha anaberekera Yakobo m’kupita kwa nthawi. Onse pamodzi analipo 7.