-
Ekisodo 18:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Koma mwa anthu onsewa, usankhe amuna oyenerera,+ oopa Mulungu,+ okhulupirika,+ odana ndi kupeza phindu mwachinyengo.+ Amenewa uwaike kukhala otsogolera anthuwa, ndipo pakhale atsogoleri a magulu a anthu 1,000,+ atsogoleri a magulu a anthu 100, atsogoleri a magulu a anthu 50 ndi atsogoleri a magulu a anthu 10.+
-
-
1 Mbiri 26:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Semaya mwana wa Obedi-edomu anabereka ana omwe anali olamulira nyumba ya bambo wawo, popeza anawo anali amuna odalirika ndi amphamvu.
-