Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mafumu 8:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Pa nthawi imeneyo Solomo+ anauza akulu,+ mitu yonse ya mafuko,+ ndi atsogoleri a makolo+ a ana a Isiraeli, kuti asonkhane+ kwa Mfumu Solomo ku Yerusalemu. Anawauza kuti akatenge likasa la pangano+ la Yehova ku Mzinda wa Davide,+ kutanthauza Ziyoni.+

  • 2 Mbiri 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pa nthawi imeneyo m’pamene Solomo anauza akulu a Isiraeli,+ mitu yonse ya mafuko,+ ndi atsogoleri a nyumba za makolo+ a ana a Isiraeli kuti asonkhane ku Yerusalemu. Anawauza kuti akatenge likasa+ la pangano la Yehova ku+ Mzinda wa Davide,+ kutanthauza Ziyoni.+

  • Salimo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Ndipo adzanena kuti: “Inetu ndakhazika mfumu yanga+

      Pa Ziyoni,+ phiri langa lopatulika.”+

  • Salimo 48:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  2 Phiri la Ziyoni limene lili m’dera lakutali la kumpoto,+

      Ndi lokongola chifukwa lili pamalo okwezeka ndi osangalatsa padziko lonse lapansi,+

      Mudzi wa Mfumu Yaikulu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena