-
1 Mbiri 24:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Semaya mwana wa Netaneli mlembi+ wa Alevi, anawalemba mayina pamaso pa mfumu, akalonga, wansembe Zadoki,+ Ahimeleki+ mwana wa Abiyatara,+ ndiponso pamaso pa atsogoleri a nyumba za makolo za ansembe ndi za Alevi.+ Anali kutenga nyumba imodzi ya makolo ya Eleazara+ ndi nyumba imodzi ya makolo ya Itamara.+
-