Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Chuma+ ndi ulemerero+ zimachokera kwa inu. Inu mumalamulira+ chilichonse. M’dzanja lanu muli mphamvu+ ndi nyonga,+ ndipo dzanja lanu limatha kukweza+ ndiponso kupereka mphamvu kwa onse.+

  • Salimo 62:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Kawiri konse ndamva kuti Mulungu wanena kuti,+

      Mphamvu ndi za Mulungu.+

  • Yesaya 14:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Pakuti Yehova wa makamu wagamula,+ ndani angazilepheretse?+ Dzanja lake n’limene latambasuka, ndani angalibweze?+

  • Yesaya 40:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Taonani! Mitundu ya anthu ili ngati dontho la madzi lochokera mumtsuko, ndipo kwa iye ili ngati fumbi pasikelo.+ Iyetu amanyamula zilumba+ ngati kuti ndi fumbi.

  • Danieli 4:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Iye amaona anthu onse okhala padziko lapansi ngati opanda pake+ ndipo amachita zinthu mogwirizana ndi chifuniro chake pakati pa makamu akumwamba ndi pakati pa anthu okhala padziko lapansi.+ Palibe aliyense amene angaletse dzanja+ lake kapena kumufunsa kuti, ‘Mukuchita chiyani?’+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena