20 Choncho Sauli ndi anthu onse amene anali naye anasonkhana pamodzi kuti apite kukamenyana ndi Afilisiti.+ Ndiyeno anayenda mpaka kukafika kumene kunali nkhondoko, ndipo anapeza kuti aphana okhaokha ndi lupanga,+ moti chipwirikiti chake chinali chosaneneka.