2 Mbiri 11:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe anachita mozindikira+ chifukwa anagawa ana akewo n’kuwaika m’madera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini.+ Anawaika m’mizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndipo anawapatsa chakudya chambiri+ ndi kuwapezera akazi ambirimbiri.+ Miyambo 13:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+
23 Komabe anachita mozindikira+ chifukwa anagawa ana akewo n’kuwaika m’madera onse a ku Yuda ndi ku Benjamini.+ Anawaika m’mizinda yonse yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri,+ ndipo anawapatsa chakudya chambiri+ ndi kuwapezera akazi ambirimbiri.+
22 Munthu wabwino adzasiyira cholowa zidzukulu zake, ndipo chuma cha wochimwa chimasungidwa kuti chidzakhale cha munthu wolungama.+