2 Mbiri 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri+ zasiliva, zagolide, zinthu zina zabwinozabwino, ndi mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndiye anali woyamba kubadwa.+
3 Bambo awo anawapatsa mphatso zambiri+ zasiliva, zagolide, zinthu zina zabwinozabwino, ndi mizinda ya ku Yuda+ yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri. Koma ufumu anaupereka kwa Yehoramu+ chifukwa ndiye anali woyamba kubadwa.+