2 Mafumu 8:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira.
20 M’masiku a Yehoramu, Aedomu+ anagalukira Yuda. Iwo anachoka m’manja mwa Yuda n’kusankha mfumu+ yoti iziwalamulira.