2 Mafumu 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 M’chaka cha 37 cha Yehoasi+ mfumu ya Yuda, Yehoasi mwana wa Yehoahazi anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 16. 2 Mafumu 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nkhani zina zokhudza Yehoasi ndi zimene anachita, ndiponso zochita zake zamphamvu, komanso mmene anamenyanirana ndi Amaziya mfumu ya Yuda, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.
10 M’chaka cha 37 cha Yehoasi+ mfumu ya Yuda, Yehoasi mwana wa Yehoahazi anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya kwa zaka 16.
15 Nkhani zina zokhudza Yehoasi ndi zimene anachita, ndiponso zochita zake zamphamvu, komanso mmene anamenyanirana ndi Amaziya mfumu ya Yuda, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Isiraeli.