2 Mafumu 15:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Uziya bambo ake anachita.+ 2 Mbiri 26:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Amaziya bambo ake anachita.+
34 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Uziya bambo ake anachita.+
4 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova,+ mogwirizana ndi zonse zimene Amaziya bambo ake anachita.+