2 Mbiri 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Uziya bambo ake anachita,+ kungoti sanakalowe m’kachisi wa Yehova.+ Koma anthu anali kuchitabe zoipa.+
2 Iye anapitiriza kuchita zoyenera pamaso pa Yehova.+ Anachita mogwirizana ndi zonse zimene Uziya bambo ake anachita,+ kungoti sanakalowe m’kachisi wa Yehova.+ Koma anthu anali kuchitabe zoipa.+