1 Mafumu 16:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+ 1 Mafumu 22:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Ahaziya+ mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya m’chaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri.
24 Kenako anagula phiri la Samariya* kwa Semeri ndi matalente* awiri a siliva. Ndiyeno anayamba kumanga mzinda paphiripo n’kuutcha dzina la Semeri mbuye wa phirilo, loti Samariya.+
51 Ahaziya+ mwana wa Ahabu anakhala mfumu ya Isiraeli ku Samariya m’chaka cha 17 cha Yehosafati mfumu ya Yuda, ndipo analamulira Isiraeli zaka ziwiri.