2 Mbiri 28:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komanso ana a Isiraeli anagwira abale awo okwana 200,000 n’kuwatenga. Pa anthu ogwidwawo panali amayi, ana aamuna ndi ana aakazi. Anafunkhanso zinthu zawo zambiri n’kupita nazo ku Samariya.+
8 Komanso ana a Isiraeli anagwira abale awo okwana 200,000 n’kuwatenga. Pa anthu ogwidwawo panali amayi, ana aamuna ndi ana aakazi. Anafunkhanso zinthu zawo zambiri n’kupita nazo ku Samariya.+