2 Mbiri 29:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero mkwiyo wa Yehova+ unayakira Yuda ndi Yerusalemu, moti anawachititsa kuti akhale chinthu chonthunthumiritsa,+ chinthu chodabwitsa,+ ndiponso chinthu chochititsa anthu kuimba mluzu,+ monga momwe mukuonera ndi maso anu.
8 Chotero mkwiyo wa Yehova+ unayakira Yuda ndi Yerusalemu, moti anawachititsa kuti akhale chinthu chonthunthumiritsa,+ chinthu chodabwitsa,+ ndiponso chinthu chochititsa anthu kuimba mluzu,+ monga momwe mukuonera ndi maso anu.