Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mafumu 16:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Tsopano guwa lansembe+ lamkuwa limene linali pamaso pa Yehova, Ahazi analichotsa kutsogolo kwa nyumbayo. Analichotsa pakati pa guwa lansembe latsopano ndi nyumba ya Yehova,+ n’kuliika kumpoto kwa guwa lake.

  • 2 Mbiri 28:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Kuwonjezera apo, Ahazi anasonkhanitsa ziwiya+ za m’nyumba ya Mulungu woona+ n’kuziphwanyaphwanya. Komanso anatseka zitseko+ za nyumba ya Yehova. Kenako anakadzimangira maguwa ansembe m’makona onse a mu Yerusalemu.+

  • 2 Mbiri 33:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Anamanga maguwa ansembe+ m’nyumba ya Yehova, imene ponena za iyo Yehova anati: “Dzina langa lidzakhala ku Yerusalemu mpaka kalekale.”+

  • 2 Mbiri 33:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso iye anaika m’nyumba ya Mulungu woona+ chifaniziro+ chimene anapanga. Koma ponena za nyumba imeneyo, Mulungu anauza Davide ndi Solomo mwana wake kuti: “M’nyumba iyi ndiponso mu Yerusalemu mzinda umene ndausankha+ pa mafuko onse a Isiraeli, ndidzaikamo dzina langa+ mpaka kalekale.+

  • 2 Mbiri 33:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye anachita zoipa pamaso pa Yehova,+ monga anachitira Manase bambo ake.+ Amoni anali kupereka nsembe+ kwa zifaniziro zonse zogoba+ zimene bambo ake+ anapanga, ndipo anapitiriza kuzitumikira.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena