Ekisodo 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mose anayankha apongozi akewo kuti: “Chifukwa anthuwa amabwera kwa ine kuti adzamve ziweruzo za Mulungu.+ 1 Samueli 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.) 1 Mafumu 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova amene watsala? Ngati alipo, tiyeni tifunsire kwa Mulungu kudzera mwa ameneyo.”+
15 Mose anayankha apongozi akewo kuti: “Chifukwa anthuwa amabwera kwa ine kuti adzamve ziweruzo za Mulungu.+
9 (Kalekale mu Isiraeli, munthu akafuna kukafunsira kwa Mulungu ankanena kuti: “Tiyeni tipite kwa wamasomphenya.”*+ Pakuti amene amatchedwa mneneri masiku ano, kalekalelo anali kutchedwa kuti wamasomphenya.)
7 Koma Yehosafati anati: “Kodi kuno kulibe mneneri wina wa Yehova amene watsala? Ngati alipo, tiyeni tifunsire kwa Mulungu kudzera mwa ameneyo.”+