Ekisodo 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kudya kwake mudzadye motere, mudzakhale mutamangirira m’chiuno mwanu,+ mutavala nsapato+ ndiponso mutatenga ndodo m’dzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi pasika* wa Yehova.+ Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova. Numeri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsopano ana a Isiraeli akonze nsembe ya pasika+ pa nthawi yake yoikidwiratu.+
11 Kudya kwake mudzadye motere, mudzakhale mutamangirira m’chiuno mwanu,+ mutavala nsapato+ ndiponso mutatenga ndodo m’dzanja lanu. Muzidzadya mofulumira. Ameneyu ndi pasika* wa Yehova.+
5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova.