2 Mbiri 35:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero anapha nyama ya pasika+ ndipo ansembe+ anawaza+ paguwa lansembe magazi amene anali kupatsidwa, pamene Alevi anali kusenda nyamazo.+
11 Atatero anapha nyama ya pasika+ ndipo ansembe+ anawaza+ paguwa lansembe magazi amene anali kupatsidwa, pamene Alevi anali kusenda nyamazo.+