1 Mafumu 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako mawu a Mulungu woona anafikira Semaya+ munthu wa Mulungu woona,+ kuti: 2 Mbiri 11:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako mawu a Yehova anafikira Semaya+ munthu wa Mulungu woona, kuti: