Numeri 31:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse. Numeri 31:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Pa hafu imene ana a Isiraeli ati alandire, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 50 zilizonse, pa anthu, ng’ombe, abulu, ndi nkhosa, ndi pa ziweto za mtundu uliwonse. Muzipereke kwa Alevi,+ amene amatumikira pachihema cha Yehova chopatulika.”+
9 Koma akazi achimidiyani ndi ana awo anawagwira ndi kuwatenga kupita nawo kwawo.+ Anafunkhanso ziweto zawo zonse ndi chuma chawo chonse.
30 Pa hafu imene ana a Isiraeli ati alandire, mutengepo chamoyo chimodzi pa zamoyo 50 zilizonse, pa anthu, ng’ombe, abulu, ndi nkhosa, ndi pa ziweto za mtundu uliwonse. Muzipereke kwa Alevi,+ amene amatumikira pachihema cha Yehova chopatulika.”+