Mlaliki 10:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+ Aheberi 12:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho limbitsani manja amene ali lende+ ndi mawondo olobodoka,+
18 Chifukwa cha ulesi waukulu denga* limaloshoka, ndipo chifukwa cha kuchita manja lende nyumba imadontha.+