2 Mafumu 17:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pamenepo mfumu ya Asuri inalamula kuti: “Mutumize wansembe mmodzi+ mwa anthu amene munawagwira. Mumutumize kuchokera kumeneko, kuti apite kukakhala m’dzikolo n’kukaphunzitsa anthuwo chipembedzo cha Mulungu wa m’dzikolo.”
27 Pamenepo mfumu ya Asuri inalamula kuti: “Mutumize wansembe mmodzi+ mwa anthu amene munawagwira. Mumutumize kuchokera kumeneko, kuti apite kukakhala m’dzikolo n’kukaphunzitsa anthuwo chipembedzo cha Mulungu wa m’dzikolo.”