Ezara 5:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koresiyo anamuuza iye kuti: “Tenga ziwiya izi.+ Pita ukaziike m’kachisi amene ali ku Yerusalemu ndipo ukaonetsetse kuti nyumba ya Mulungu yamangidwanso pamalo ake.”+
15 Koresiyo anamuuza iye kuti: “Tenga ziwiya izi.+ Pita ukaziike m’kachisi amene ali ku Yerusalemu ndipo ukaonetsetse kuti nyumba ya Mulungu yamangidwanso pamalo ake.”+