-
1 Samueli 11:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Iye anatenga ng’ombe ziwiri zamphongo n’kuziduladula. Kenako anatumiza amithenga kukapereka zigawo za ng’ombezo m’dziko lonse la Isiraeli+ ndipo anati: “Aliyense amene satsatira Sauli ndi Samueli, izi n’zimene zichitikire ng’ombe zake.”+ Anthu atamva mawu amenewa anagwidwa ndi mantha+ ochokera kwa Yehova,+ moti onse anapita mogwirizana.+
-