Oweruza 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kenako ana a Isiraeli anati: “Ndani mwa mafuko onse a Isiraeli amene sanabwere kwa Yehova pamodzi ndi mpingo wonse? Pajatu tinachita lumbiro lalikulu+ lokhudza aliyense amene sanabwere kwa Yehova ku Mizipa, lakuti: ‘Ameneyo aphedwe ndithu.’”+
5 Kenako ana a Isiraeli anati: “Ndani mwa mafuko onse a Isiraeli amene sanabwere kwa Yehova pamodzi ndi mpingo wonse? Pajatu tinachita lumbiro lalikulu+ lokhudza aliyense amene sanabwere kwa Yehova ku Mizipa, lakuti: ‘Ameneyo aphedwe ndithu.’”+