Mlaliki 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Mitsinje*+ yonse imapita kunyanja+ koma nyanjayo sidzaza.+ Mitsinjeyo imabwerera kumalo kumene inachokera kuti ikayambirenso kuyenda.+
7 Mitsinje*+ yonse imapita kunyanja+ koma nyanjayo sidzaza.+ Mitsinjeyo imabwerera kumalo kumene inachokera kuti ikayambirenso kuyenda.+