Deuteronomo 7:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+ Ezara 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pomalizira pake, pofika pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, anamaliza kufufuza amuna onse amene anatenga akazi achilendo.+ 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
3 Usadzachite nawo mgwirizano wa ukwati. Usadzapereke ana ako aakazi kwa ana awo aamuna ndipo usadzatenge ana awo aakazi ndi kuwapereka kwa ana ako aamuna.+
17 Pomalizira pake, pofika pa tsiku loyamba la mwezi woyamba, anamaliza kufufuza amuna onse amene anatenga akazi achilendo.+
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+