Ezara 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Aliyense wosatsatira chilamulo cha Mulungu wako+ ndi chilamulo cha mfumu, azipatsidwa chiweruzo msangamsanga, kaya choti aphedwe,+ athamangitsidwe,+ alipitsidwe ndalama,+ kapena aikidwe m’ndende.” Aroma 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda. 1 Petulo 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kapena nduna chifukwa n’zotumidwa ndi mfumuyo kuti zizipereka chilango kwa ochita zoipa ndi kuyamikira ochita zabwino.+
26 Aliyense wosatsatira chilamulo cha Mulungu wako+ ndi chilamulo cha mfumu, azipatsidwa chiweruzo msangamsanga, kaya choti aphedwe,+ athamangitsidwe,+ alipitsidwe ndalama,+ kapena aikidwe m’ndende.”
3 Pakuti olamulira amaopsa ngati ukuchita zoipa,+ osati ngati ukuchita zabwino. Choncho kodi ukufuna kuti usamachite mantha ndi olamulira? Pitiriza kuchita zabwino,+ ndipo olamulira adzakutamanda.
14 kapena nduna chifukwa n’zotumidwa ndi mfumuyo kuti zizipereka chilango kwa ochita zoipa ndi kuyamikira ochita zabwino.+