-
Nehemiya 3:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Kenako Uziyeli mwana wamwamuna wa Harihaya, mmodzi wa osula golide,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene winayo analekezera. Ndiyeno Hananiya mmodzi wa opanga mafuta onunkhira,+ anakonza mpandawo kuchokera pamene Uziyeli analekezera. Iwo anayala miyala mu Yerusalemu mpaka kukafika ku Khoma Lalikulu.+
-