Nehemiya 3:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Malikiya amene anali m’gulu la osula golide,+ anakonza mpandawo mpaka kukafika kunyumba ya Anetini+ ndi amalonda,+ kutsogolo kwa Chipata cha Kufufuza* mpaka pachipinda chapadenga cha pakona.
31 Malikiya amene anali m’gulu la osula golide,+ anakonza mpandawo mpaka kukafika kunyumba ya Anetini+ ndi amalonda,+ kutsogolo kwa Chipata cha Kufufuza* mpaka pachipinda chapadenga cha pakona.